Mateyu 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chenjerani ndi anthu,+ pakuti adzakuperekani kumakhoti aang’ono,+ ndipo adzakukwapulani+ m’masunagoge awo.+ 1 Petulo 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipotu, pa chifukwa chimenechi uthenga wabwino unalengezedwanso kwa akufa,+ kuti aweruzidwe mwa thupi mogwirizana ndi kuona kwa anthu,+ koma akhale ndi moyo mwa mzimu+ mogwirizana ndi kuona kwa Mulungu.
17 Chenjerani ndi anthu,+ pakuti adzakuperekani kumakhoti aang’ono,+ ndipo adzakukwapulani+ m’masunagoge awo.+
6 Ndipotu, pa chifukwa chimenechi uthenga wabwino unalengezedwanso kwa akufa,+ kuti aweruzidwe mwa thupi mogwirizana ndi kuona kwa anthu,+ koma akhale ndi moyo mwa mzimu+ mogwirizana ndi kuona kwa Mulungu.