Yeremiya 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ‘Ndithudi, monga mmene mkazi amasiyira mwamuna wake+ mwachinyengo, inunso a m’nyumba ya Isiraeli mwandichitira zachinyengo,’+ watero Yehova.” Mateyu 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero salinso awiri, koma thupi limodzi. Choncho chimene Mulungu wachimanga pamodzi, munthu asachilekanitse.”+ Maliko 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye anawauza kuti: “Aliyense wosiya mkazi wake ndi kukwatira wina, wachita chigololo+ molakwira mkaziyo. Luka 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Aliyense wosiya mkazi wake ndi kukwatira wina, wachita chigololo, ndipo wokwatira mkazi wosiyidwayo wachita chigololo.+
20 ‘Ndithudi, monga mmene mkazi amasiyira mwamuna wake+ mwachinyengo, inunso a m’nyumba ya Isiraeli mwandichitira zachinyengo,’+ watero Yehova.”
6 Chotero salinso awiri, koma thupi limodzi. Choncho chimene Mulungu wachimanga pamodzi, munthu asachilekanitse.”+
11 Iye anawauza kuti: “Aliyense wosiya mkazi wake ndi kukwatira wina, wachita chigololo+ molakwira mkaziyo.
18 “Aliyense wosiya mkazi wake ndi kukwatira wina, wachita chigololo, ndipo wokwatira mkazi wosiyidwayo wachita chigololo.+