2 Akorinto 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Sitikuchita chilichonse chokhumudwitsa,+ kuti utumiki wathu usapezedwe chifukwa.+ 2 Akorinto 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kapena kodi ndinachita tchimo pamene ndinadzichepetsa+ kuti inuyo mukwezedwe, muja ndinalengeza mosangalala uthenga wabwino wa Mulungu kwa inu, popanda inuyo kutayirapo ndalama?+
7 Kapena kodi ndinachita tchimo pamene ndinadzichepetsa+ kuti inuyo mukwezedwe, muja ndinalengeza mosangalala uthenga wabwino wa Mulungu kwa inu, popanda inuyo kutayirapo ndalama?+