Genesis 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kwa mkaziyo, Mulungu ananena kuti: “Ndidzawonjezera kuvutika kwako pamene uli ndi pakati.+ Pobereka ana udzamva zowawa.+ Udzakhumba mwamuna wako, ndipo iye adzakulamulira.”+ Yobu 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Munthu wobadwa kwa mkazi,+Amakhala ndi moyo waufupi,+ wodzaza ndi masautso.+
16 Kwa mkaziyo, Mulungu ananena kuti: “Ndidzawonjezera kuvutika kwako pamene uli ndi pakati.+ Pobereka ana udzamva zowawa.+ Udzakhumba mwamuna wako, ndipo iye adzakulamulira.”+