Aheberi 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mulungu nayenso anachitira umboni za chipulumutsocho ndi zizindikiro, zinthu zodabwitsa, ntchito zamphamvu zosiyanasiyana+ komanso mwa kupereka mphatso zosiyanasiyana+ za mzimu woyera malinga ndi chifuniro chake.+ 1 Petulo 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Molingana ndi mphatso imene aliyense walandira, igwiritseni ntchito potumikirana monga oyang’anira abwino amene alandira kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu, kumene wakusonyeza m’njira zosiyanasiyana.+
4 Mulungu nayenso anachitira umboni za chipulumutsocho ndi zizindikiro, zinthu zodabwitsa, ntchito zamphamvu zosiyanasiyana+ komanso mwa kupereka mphatso zosiyanasiyana+ za mzimu woyera malinga ndi chifuniro chake.+
10 Molingana ndi mphatso imene aliyense walandira, igwiritseni ntchito potumikirana monga oyang’anira abwino amene alandira kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu, kumene wakusonyeza m’njira zosiyanasiyana.+