1 Akorinto 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Chifukwa wolankhula lilime lachilendo salankhula ndi anthu, koma ndi Mulungu, pakuti palibe amene amamva zonena zake,+ koma amalankhula zinsinsi zopatulika+ mwa mzimu.
2 Chifukwa wolankhula lilime lachilendo salankhula ndi anthu, koma ndi Mulungu, pakuti palibe amene amamva zonena zake,+ koma amalankhula zinsinsi zopatulika+ mwa mzimu.