Ekisodo 31:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno atamaliza kulankhula naye paphiri la Sinai, anapatsa Mose miyala iwiri yosema ya Umboni,+ miyala yolembedwapo mawu ndi chala cha Mulungu.+ Ekisodo 32:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Miyalayo inapangidwa ndi Mulungu, ndipo mawuwo analembedwapo ndi Mulungu mochita kugoba.+
18 Ndiyeno atamaliza kulankhula naye paphiri la Sinai, anapatsa Mose miyala iwiri yosema ya Umboni,+ miyala yolembedwapo mawu ndi chala cha Mulungu.+