Yeremiya 31:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nditabwerera kwa inu ndinadzimvera chisoni.+ Mutandithandiza kuzindikira ndinadzimenya pantchafu chifukwa cha chisoni.+ Ndinachita manyazi ndipo ndinanyazitsidwa+ chifukwa cha chitonzo cha paubwana wanga.’”+ Machitidwe 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma kuyambira kwa okhala ku Damasiko+ ndi ku Yerusalemu,+ komanso m’dziko lonse la Yudeya ndi kwa anthu a mitundu ina,+ ndinafikitsa uthenga wakuti alape ndi kutembenukira kwa Mulungu mwa kuchita ntchito zosonyeza kulapa.+
19 Nditabwerera kwa inu ndinadzimvera chisoni.+ Mutandithandiza kuzindikira ndinadzimenya pantchafu chifukwa cha chisoni.+ Ndinachita manyazi ndipo ndinanyazitsidwa+ chifukwa cha chitonzo cha paubwana wanga.’”+
20 Koma kuyambira kwa okhala ku Damasiko+ ndi ku Yerusalemu,+ komanso m’dziko lonse la Yudeya ndi kwa anthu a mitundu ina,+ ndinafikitsa uthenga wakuti alape ndi kutembenukira kwa Mulungu mwa kuchita ntchito zosonyeza kulapa.+