2 Akorinto 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndikuopa kuti mwinamwake ndikadzafika,+ sindidzakupezani mmene ndikanafunira. Kwa inunso sindidzakhala mmene mukanafunira. M’malomwake, ndidzapeza ndewu, nsanje,+ kukwiyitsana, mikangano, miseche, manong’onong’o, kudzitukumula, ndi zisokonezo.+ 2 Akorinto 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ngakhale kuti panopa ndili kutali ndi inu, koma muone mawu angawa ngati kuti ndili limodzi nanu kachiwiri. Choncho, monga mmene ndinachitira kale, ndikuchenjeza anthu amene anachimwa, komanso ena onse, kuti ndikadzabweranso kumeneko sindidzalekerera munthu.+
20 Ndikuopa kuti mwinamwake ndikadzafika,+ sindidzakupezani mmene ndikanafunira. Kwa inunso sindidzakhala mmene mukanafunira. M’malomwake, ndidzapeza ndewu, nsanje,+ kukwiyitsana, mikangano, miseche, manong’onong’o, kudzitukumula, ndi zisokonezo.+
2 Ngakhale kuti panopa ndili kutali ndi inu, koma muone mawu angawa ngati kuti ndili limodzi nanu kachiwiri. Choncho, monga mmene ndinachitira kale, ndikuchenjeza anthu amene anachimwa, komanso ena onse, kuti ndikadzabweranso kumeneko sindidzalekerera munthu.+