Afilipi 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti ena onse akungofuna za iwo eni,+ osati za Khristu Yesu. 2 Yohane 10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wina akabwera kwa inu ndi chiphunzitso chosiyana ndi ichi, musamulandire m’nyumba zanu+ kapena kumupatsa moni.+
10 Wina akabwera kwa inu ndi chiphunzitso chosiyana ndi ichi, musamulandire m’nyumba zanu+ kapena kumupatsa moni.+