Aroma 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mulungu, amene ndikumuchitira utumiki wopatulika ndi moyo wanga wonse polalikira uthenga wabwino wonena za Mwana wake, ndiye mboni yanga+ ya mmene ndimakutchulirani m’mapemphero anga nthawi zonse.+ Afilipi 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndimachita zimenezi m’pembedzero langa lililonse limene ndimapereka mosangalala chifukwa cha nonsenu.+ Afilipi 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo ine ndikupitiriza kupemphera kuti chikondi chanu chipitirire kukula,+ limodzi ndi kudziwa zinthu molondola,+ komanso kuzindikira zinthu bwino kwambiri.+ Akolose 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nthawi zonse tikamakupemphererani,+ timayamika+ Mulungu, Atate wa Ambuye wathu Yesu Khristu. 1 Atesalonika 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nthawi zonse timayamika Mulungu tikamatchula za inu nonse m’mapemphero athu.+
9 Mulungu, amene ndikumuchitira utumiki wopatulika ndi moyo wanga wonse polalikira uthenga wabwino wonena za Mwana wake, ndiye mboni yanga+ ya mmene ndimakutchulirani m’mapemphero anga nthawi zonse.+
4 Ndimachita zimenezi m’pembedzero langa lililonse limene ndimapereka mosangalala chifukwa cha nonsenu.+
9 Ndipo ine ndikupitiriza kupemphera kuti chikondi chanu chipitirire kukula,+ limodzi ndi kudziwa zinthu molondola,+ komanso kuzindikira zinthu bwino kwambiri.+