Aheberi 10:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pakuti mukufunika kupirira,+ kuti mutachita chifuniro cha Mulungu,+ mudzalandire zimene Mulungu walonjeza.+ 2 Yohane 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Samalani kuti musalephere kulandira mphoto ya zinthu zimene tazigwirira kale ntchito, kuti mudzalandire mphoto yokwanira.+
36 Pakuti mukufunika kupirira,+ kuti mutachita chifuniro cha Mulungu,+ mudzalandire zimene Mulungu walonjeza.+
8 Samalani kuti musalephere kulandira mphoto ya zinthu zimene tazigwirira kale ntchito, kuti mudzalandire mphoto yokwanira.+