2 Akorinto 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kulikonse kumene tikupita, timapirira m’matupi mwathu ndipo timakhala pa ngozi yoti tikhoza kuphedwa, ngati mmene Yesu anachitira,+ kuti moyo wa Yesu uonekerenso m’matupi mwathu.+ Afilipi 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndachita zimenezi kuti ndim’dziwe komanso kuti ndidziwe mphamvu ya kuuka kwake kwa akufa.+ Kutinso ndigawane naye m’masautso+ ake, ndi kulolera kufa imfa monga yake.+
10 Kulikonse kumene tikupita, timapirira m’matupi mwathu ndipo timakhala pa ngozi yoti tikhoza kuphedwa, ngati mmene Yesu anachitira,+ kuti moyo wa Yesu uonekerenso m’matupi mwathu.+
10 Ndachita zimenezi kuti ndim’dziwe komanso kuti ndidziwe mphamvu ya kuuka kwake kwa akufa.+ Kutinso ndigawane naye m’masautso+ ake, ndi kulolera kufa imfa monga yake.+