1 Atesalonika 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Akufunanso kuti aliyense wa inu akhale woyera mwa kudziwa kulamulira thupi lake+ m’njira yoyera+ kuti mukhale olemekezeka pamaso pa Mulungu, Aheberi 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti mkulu wa ansembe ngati ameneyu ndiyedi wotiyenerera.+ Iye ndi wokhulupirika,+ wosalakwa,+ wosaipitsidwa,+ wosiyana ndi anthu ochimwa,+ ndipo wakwera pamwamba kwambiri kuposa kumwamba.+
4 Akufunanso kuti aliyense wa inu akhale woyera mwa kudziwa kulamulira thupi lake+ m’njira yoyera+ kuti mukhale olemekezeka pamaso pa Mulungu,
26 Pakuti mkulu wa ansembe ngati ameneyu ndiyedi wotiyenerera.+ Iye ndi wokhulupirika,+ wosalakwa,+ wosaipitsidwa,+ wosiyana ndi anthu ochimwa,+ ndipo wakwera pamwamba kwambiri kuposa kumwamba.+