Machitidwe 10:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mulungu anatumiza mawu+ kwa ana a Isiraeli ndi kulengeza kwa iwo uthenga wabwino wa mtendere+ kudzera mwa Yesu Khristu. Ameneyu ndiye Ambuye wa ena onse.+ Aroma 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo angalalikire bwanji ngati sanatumidwe?+ Zili monga muja Malemba amanenera kuti: “Mapazi a anthu olengeza uthenga wabwino wa zinthu zabwino, ndi okongola kwabasi!”+
36 Mulungu anatumiza mawu+ kwa ana a Isiraeli ndi kulengeza kwa iwo uthenga wabwino wa mtendere+ kudzera mwa Yesu Khristu. Ameneyu ndiye Ambuye wa ena onse.+
15 Ndipo angalalikire bwanji ngati sanatumidwe?+ Zili monga muja Malemba amanenera kuti: “Mapazi a anthu olengeza uthenga wabwino wa zinthu zabwino, ndi okongola kwabasi!”+