Aroma 8:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiponso, amene anawasankhiratu+ ndi amenenso anawaitana,+ ndipo amene anawaitanawo ndi amenenso anawayesa olungama.+ Kenako amene anawayesa olungama ndi amenenso anawapatsa ulemerero.+ Aheberi 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero, abale athu oyera, amene muli nawo m’gulu la oitanidwa kumwamba,+ ganizirani za Yesu, mtumwi+ ndi mkulu wa ansembe amene tikumuvomereza.+
30 Ndiponso, amene anawasankhiratu+ ndi amenenso anawaitana,+ ndipo amene anawaitanawo ndi amenenso anawayesa olungama.+ Kenako amene anawayesa olungama ndi amenenso anawapatsa ulemerero.+
3 Chotero, abale athu oyera, amene muli nawo m’gulu la oitanidwa kumwamba,+ ganizirani za Yesu, mtumwi+ ndi mkulu wa ansembe amene tikumuvomereza.+