1 Akorinto 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mpaka pano tikadali anjala+ ndi aludzu+ ndi ausiwa.+ Tikuzunzidwabe,+ tikusowabe pokhala,+ 2 Akorinto 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ngati ogwidwa ndi chisoni koma osangalala nthawi zonse, ngati osauka koma olemeretsa anthu ambiri, ngati opanda kalikonse koma okhala ndi zinthu zonse.+
10 ngati ogwidwa ndi chisoni koma osangalala nthawi zonse, ngati osauka koma olemeretsa anthu ambiri, ngati opanda kalikonse koma okhala ndi zinthu zonse.+