Deuteronomo 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mitima yanu muichite mdulidwe+ ndipo musakhalenso ouma khosi.+ Aroma 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma Myuda ndi amene ali wotero mkati,+ ndipo mdulidwe wake ndi wa mumtima+ wochitidwa ndi mzimu, osati ndi malamulo olembedwa.+ Munthu woteroyo satamandidwa+ ndi anthu koma ndi Mulungu.+ Afilipi 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ife ndife amdulidwe weniweni,+ amene tikuchita utumiki wopatulika mwa mzimu wa Mulungu.+ Timadzitamandira mwa Khristu Yesu,+ ndipo sitidalira zinthu zimene anthu amaziona kuti ndi zofunika,+
29 Koma Myuda ndi amene ali wotero mkati,+ ndipo mdulidwe wake ndi wa mumtima+ wochitidwa ndi mzimu, osati ndi malamulo olembedwa.+ Munthu woteroyo satamandidwa+ ndi anthu koma ndi Mulungu.+
3 Pakuti ife ndife amdulidwe weniweni,+ amene tikuchita utumiki wopatulika mwa mzimu wa Mulungu.+ Timadzitamandira mwa Khristu Yesu,+ ndipo sitidalira zinthu zimene anthu amaziona kuti ndi zofunika,+