Salimo 68:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwo aona magulu anu a anthu opambana akuyendera pamodzi, inu Mulungu,+Magulu a anthu oyendera pamodzi a Mulungu wanga, Mfumu yanga, akukalowa kumalo oyera.+ 2 Akorinto 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma tiyamike Mulungu amene nthawi zonse amatitsogolera+ pamodzi ndi Khristu ngati kuti tikuguba pa chionetsero chonyadirira kupambana.+ Kudziwa Mulungu kuli ngati fungo lonunkhira bwino ndipo kudzera mu ntchito yathu fungoli likufalikira paliponse.+
24 Iwo aona magulu anu a anthu opambana akuyendera pamodzi, inu Mulungu,+Magulu a anthu oyendera pamodzi a Mulungu wanga, Mfumu yanga, akukalowa kumalo oyera.+
14 Koma tiyamike Mulungu amene nthawi zonse amatitsogolera+ pamodzi ndi Khristu ngati kuti tikuguba pa chionetsero chonyadirira kupambana.+ Kudziwa Mulungu kuli ngati fungo lonunkhira bwino ndipo kudzera mu ntchito yathu fungoli likufalikira paliponse.+