Yohane 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye anali m’dziko,+ ndipo dziko linakhalapo kudzera mwa iye.+ Koma dzikolo silinamudziwe. Aheberi 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumapeto kwa masiku ano,+ iye walankhulanso kwa ife kudzera mwa Mwana wake,+ amene anamuika kuti akhale wolandira zinthu zonse monga cholowa.+ Kudzera mwa iyeyu, Mulungu analenga+ nthawi* zosiyanasiyana.
2 Kumapeto kwa masiku ano,+ iye walankhulanso kwa ife kudzera mwa Mwana wake,+ amene anamuika kuti akhale wolandira zinthu zonse monga cholowa.+ Kudzera mwa iyeyu, Mulungu analenga+ nthawi* zosiyanasiyana.