Salimo 94:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 94 Inu Yehova, Mulungu wobwezera anthu oipa,+Inu Mulungu wobwezera anthu oipa, walani!+ 2 Atesalonika 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa nthawi imeneyo adzabwezera chilango+ kwa anthu osadziwa Mulungu+ ndi kwa anthu osamvera uthenga wabwino+ wonena za Ambuye wathu Yesu.+
8 Pa nthawi imeneyo adzabwezera chilango+ kwa anthu osadziwa Mulungu+ ndi kwa anthu osamvera uthenga wabwino+ wonena za Ambuye wathu Yesu.+