Machitidwe 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo anthu amene anaperekeza Paulo anakamufikitsa ku Atene. Koma anabwerera atatumidwa kuti akauze Sila ndi Timoteyo+ kuti amutsatire msanga.
15 Ndipo anthu amene anaperekeza Paulo anakamufikitsa ku Atene. Koma anabwerera atatumidwa kuti akauze Sila ndi Timoteyo+ kuti amutsatire msanga.