1 Akorinto 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano landirani moni wanga wolemba ndekha ndi dzanja langa, ineyo Paulo.+ Akolose 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano landirani moni wanga wolemba ndekha ndi dzanja langa,+ ineyo Paulo. Pitirizani kukumbukira maunyolo+ amene andimanga nawo kundende kuno. Kukoma mtima kwakukulu kukhale nanu.
18 Tsopano landirani moni wanga wolemba ndekha ndi dzanja langa,+ ineyo Paulo. Pitirizani kukumbukira maunyolo+ amene andimanga nawo kundende kuno. Kukoma mtima kwakukulu kukhale nanu.