Machitidwe 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero abale, fufuzani+ pakati panu amuna 7 a mbiri yabwino, amene ali ndi mzimu komanso nzeru zochuluka,+ kuti ife tiwaike kukhala oyang’anira ntchito yofunikayi. Tito 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti woyang’anira ayenera kukhala wopanda chifukwa chomunenezera.+ Pokhala mtumiki*+ wa Mulungu, asakhale womva zake zokha,+ wa mtima wapachala,+ womwa mowa mwauchidakwa,*+ wandewu,+ kapena wokonda kupeza phindu mwachinyengo.+ 1 Petulo 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Wetani+ gulu la nkhosa za Mulungu+ lomwe analisiya m’manja mwanu, osati mokakamizika, koma mofunitsitsa.+ Osatinso chifukwa chofuna kupindulapo kenakake,+ koma ndi mtima wonse.
3 Chotero abale, fufuzani+ pakati panu amuna 7 a mbiri yabwino, amene ali ndi mzimu komanso nzeru zochuluka,+ kuti ife tiwaike kukhala oyang’anira ntchito yofunikayi.
7 Pakuti woyang’anira ayenera kukhala wopanda chifukwa chomunenezera.+ Pokhala mtumiki*+ wa Mulungu, asakhale womva zake zokha,+ wa mtima wapachala,+ womwa mowa mwauchidakwa,*+ wandewu,+ kapena wokonda kupeza phindu mwachinyengo.+
2 Wetani+ gulu la nkhosa za Mulungu+ lomwe analisiya m’manja mwanu, osati mokakamizika, koma mofunitsitsa.+ Osatinso chifukwa chofuna kupindulapo kenakake,+ koma ndi mtima wonse.