Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 4:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndiponso chipulumutso sichipezeka mwa munthu wina aliyense, pakuti palibe dzina lina+ pansi pa thambo, limene laperekedwa kwa anthu, limene tiyenera kupulumutsidwa nalo.”+

  • Aroma 5:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma mmene zilili ndi mphatsoyi si mmene zinalili ndi uchimowo. Popeza ngati mwa uchimo wa munthu mmodzi ambiri anafa, kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu ndiponso mphatso yake yaulere zinasefukira kwa anthu ambiri.+ Mphatso yaulere imeneyi inaperekedwa limodzi ndi kukoma mtima kwakukulu kudzera mwa munthu mmodzi,+ Yesu Khristu.

  • Akolose 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiponso, ngakhale kuti munali akufa m’machimo anu ndipo munali osadulidwa, Mulungu anakupatsani moyo kuti mukhale ogwirizana ndi Khristu,+ ndipo anatikhululukira machimo athu onse motikomera mtima.+

  • 2 Timoteyo 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma tsopano izi zatsimikizirika bwino chifukwa cha kuonekera+ kwa Mpulumutsi wathu Khristu Yesu, amene wathetsa mphamvu imfa.+ Kudzera mu uthenga wabwino,+ iye watidziwitsa bwinobwino+ mmene tingapezere moyo+ wosawonongeka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena