Yesaya 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndikuika mwala mu Ziyoni+ kuti ukhale maziko. Umenewu ndi mwala+ wapakona woyesedwa,+ wamtengo wapatali,+ woti ukhale maziko olimba.+ Palibe munthu woukhulupirira amene adzade nkhawa.+ Aheberi 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti anali kuyembekezera mzinda+ wokhala ndi maziko enieni, mzinda umene Mulungu ndiye anaumanga ndi kuupanga.+
16 Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ndikuika mwala mu Ziyoni+ kuti ukhale maziko. Umenewu ndi mwala+ wapakona woyesedwa,+ wamtengo wapatali,+ woti ukhale maziko olimba.+ Palibe munthu woukhulupirira amene adzade nkhawa.+
10 Pakuti anali kuyembekezera mzinda+ wokhala ndi maziko enieni, mzinda umene Mulungu ndiye anaumanga ndi kuupanga.+