Numeri 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Mose analankhula ndi Kora ndiponso khamu lonselo, kuti: “Mawa m’mawa, Yehova aonetsa amene ali wake+ ndiponso amene ali woyera.+ Aonetsa amene ayenera kuima pamaso pake,+ ndipo amene ati am’sankheyo+ adzaima pamaso pake. 1 Akorinto 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma ngati munthu akukonda Mulungu,+ ameneyo amadziwika kwa Mulungu.+
5 Ndiyeno Mose analankhula ndi Kora ndiponso khamu lonselo, kuti: “Mawa m’mawa, Yehova aonetsa amene ali wake+ ndiponso amene ali woyera.+ Aonetsa amene ayenera kuima pamaso pake,+ ndipo amene ati am’sankheyo+ adzaima pamaso pake.