Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Yesu anayankha kuti: “Ndithudi ndikukuuza, Munthu sangathe kulowa mu ufumu wa Mulungu atapanda kubadwa mwa madzi+ ndi mzimu.+

  • Aroma 8:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Onse amene akutsogoleredwa ndi mzimu wa Mulungu, amenewa ndiwo ana a Mulungu.+

  • Aroma 8:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Si zokhazo ayi, komanso ifeyo amene tili ndi zipatso zoyambirira+ zomwe ndi mzimu, tikubuula+ mumtima mwathu pamene tikudikira ndi mtima wonse kuti titengedwe kukhala ana a Mulungu,+ kumasulidwa ndi dipo* kuti tituluke m’matupi athu.

  • 2 Akorinto 5:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho ngati aliyense ali wogwirizana ndi Khristu, iye ndi cholengedwa chatsopano.+ Zinthu zakale zinatha,+ ndipo pali zatsopano.+

  • Aheberi 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pali anthu amene Mulungu anawaunikira,+ amene analawa mphatso yaulere yakumwamba,+ amene analandira mzimu woyera,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena