Yeremiya 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova wanena kuti: “Kodi mawu anga safanana ndi moto?+ Kodi safanana ndi nyundo imene imaphwanya thanthwe?”+ Zekariya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho iye anandiuza kuti: “Yehova wauza Zerubabele kuti, ‘“Kuti zinthu zonsezi zichitike, sipakufunika gulu lankhondo,+ kapena mphamvu,+ koma mzimu wanga,”+ watero Yehova wa makamu. Yohane 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo ophunzira ake anakumbukira zimene Malemba amanena, kuti amati: “Kudzipereka kwambiri panyumba yanu kudzandidya.”+ 1 Petulo 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti inu mwabadwa mwatsopano,+ osati kuchokera m’mbewu yotha kuwonongeka,+ koma m’mbewu+ yosatha kuwonongeka,+ kudzera m’mawu+ a Mulungu wamoyo ndi wamuyaya.+
29 Yehova wanena kuti: “Kodi mawu anga safanana ndi moto?+ Kodi safanana ndi nyundo imene imaphwanya thanthwe?”+
6 Choncho iye anandiuza kuti: “Yehova wauza Zerubabele kuti, ‘“Kuti zinthu zonsezi zichitike, sipakufunika gulu lankhondo,+ kapena mphamvu,+ koma mzimu wanga,”+ watero Yehova wa makamu.
17 Pamenepo ophunzira ake anakumbukira zimene Malemba amanena, kuti amati: “Kudzipereka kwambiri panyumba yanu kudzandidya.”+
23 Pakuti inu mwabadwa mwatsopano,+ osati kuchokera m’mbewu yotha kuwonongeka,+ koma m’mbewu+ yosatha kuwonongeka,+ kudzera m’mawu+ a Mulungu wamoyo ndi wamuyaya.+