Akolose 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anafafanizanso+ chikalata cholembedwa ndi manja,+ chokhala ndi malamulo+ operekedwa monga malangizo, chimene chinali kutitsutsa.+ Ndipo Iye wachichotsa mwa kuchikhomera+ pamtengo wozunzikirapo.*+ Aheberi 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ponena kuti “pangano latsopano,” iye wapanga loyambalo kukhala lotha ntchito.+ Tsopano pangano limene latha ntchito ndipo likukalamba, latsala pang’ono kufafanizika.+
14 Anafafanizanso+ chikalata cholembedwa ndi manja,+ chokhala ndi malamulo+ operekedwa monga malangizo, chimene chinali kutitsutsa.+ Ndipo Iye wachichotsa mwa kuchikhomera+ pamtengo wozunzikirapo.*+
13 Ponena kuti “pangano latsopano,” iye wapanga loyambalo kukhala lotha ntchito.+ Tsopano pangano limene latha ntchito ndipo likukalamba, latsala pang’ono kufafanizika.+