Salimo 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndimaganiza kuti: Munthu+ ndani kuti muzimuganizira,+Ndipo mwana wa munthu wochokera kufumbi ndani kuti muzimusamalira?+ Salimo 144:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, munthu ndani kuti mumuganizire?+Kodi mwana wa munthu wochokera kufumbi+ ndani kuti mumuwerengere?
4 Ndimaganiza kuti: Munthu+ ndani kuti muzimuganizira,+Ndipo mwana wa munthu wochokera kufumbi ndani kuti muzimusamalira?+
3 Inu Yehova, munthu ndani kuti mumuganizire?+Kodi mwana wa munthu wochokera kufumbi+ ndani kuti mumuwerengere?