2 Samueli 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mzimu wa Yehova unandilankhulitsa,+Ndipo mawu ake anali palilime langa.+ Machitidwe 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Amuna inu, abale, kudzera pakamwa pa Davide, mzimu woyera+ unaneneratu lemba lokhudza Yudasi,+ amene anatsogolera anthu okagwira Yesu.+ Kunali kofunikira kuti lembalo likwaniritsidwe+
16 “Amuna inu, abale, kudzera pakamwa pa Davide, mzimu woyera+ unaneneratu lemba lokhudza Yudasi,+ amene anatsogolera anthu okagwira Yesu.+ Kunali kofunikira kuti lembalo likwaniritsidwe+