Salimo 41:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma munthu amene ndinali kukhala naye mwamtendere, amene ndinali kumukhulupirira,+Munthu amene anali kudya chakudya changa,+ wakweza chidendene chake kundiukira.+ Salimo 55:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti amene ananditonza si mdani.+Akanakhala mdani ndikanapirira.Amene anadzikweza pamaso panga si munthu wodana nane kwambiri.+Akanakhala munthu wodana nane kwambiri ndikanabisala.+ Luka 22:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Mawu adakali m’kamwa, panafika khamu la anthu, limodzi ndi Yudasi, mmodzi wa ophunzira 12 aja, akuwatsogolera.+ Ndiyeno Yudasi anapita pamene panali Yesu kukamupsompsona.+
9 Koma munthu amene ndinali kukhala naye mwamtendere, amene ndinali kumukhulupirira,+Munthu amene anali kudya chakudya changa,+ wakweza chidendene chake kundiukira.+
12 Pakuti amene ananditonza si mdani.+Akanakhala mdani ndikanapirira.Amene anadzikweza pamaso panga si munthu wodana nane kwambiri.+Akanakhala munthu wodana nane kwambiri ndikanabisala.+
47 Mawu adakali m’kamwa, panafika khamu la anthu, limodzi ndi Yudasi, mmodzi wa ophunzira 12 aja, akuwatsogolera.+ Ndiyeno Yudasi anapita pamene panali Yesu kukamupsompsona.+