Aheberi 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tisaleke kusonkhana pamodzi,+ monga mmene ena achizolowezi chosafika pamisonkhano akuchitira. Koma tiyeni tilimbikitsane,+ ndipo tiwonjezere kuchita zimenezi, makamaka pamene mukuona kuti tsikulo likuyandikira.+
25 Tisaleke kusonkhana pamodzi,+ monga mmene ena achizolowezi chosafika pamisonkhano akuchitira. Koma tiyeni tilimbikitsane,+ ndipo tiwonjezere kuchita zimenezi, makamaka pamene mukuona kuti tsikulo likuyandikira.+