1 Timoteyo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndiponso kuti asamamvere nkhani zonama+ ndi kukumbana mibadwo ya makolo. Zimenezi n’zosapindulitsa,+ koma zimangoyambitsa mafunso ndipo siziphunzitsa anthu chilichonse chochokera kwa Mulungu chokhudza chikhulupiriro.
4 ndiponso kuti asamamvere nkhani zonama+ ndi kukumbana mibadwo ya makolo. Zimenezi n’zosapindulitsa,+ koma zimangoyambitsa mafunso ndipo siziphunzitsa anthu chilichonse chochokera kwa Mulungu chokhudza chikhulupiriro.