Mateyu 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumeneko iye anasandulika pamaso pawo, ndipo nkhope yake inawala ngati dzuwa.+ Malaya ake akunja anawala kwambiri.+ Maliko 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Malinga ndi zimenezo, patapita masiku 6, Yesu anatenga Petulo, Yakobo ndi Yohane, n’kukwera nawo m’phiri lalitali, kwaokhaokha. Kumeneko iye anasandulika pamaso pawo,+ Luka 9:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamene anali kupemphera, maonekedwe+ a nkhope yake anasintha ndipo chovala chake chinaoneka choyera kwambiri ndi chonyezimira.+
2 Kumeneko iye anasandulika pamaso pawo, ndipo nkhope yake inawala ngati dzuwa.+ Malaya ake akunja anawala kwambiri.+
2 Malinga ndi zimenezo, patapita masiku 6, Yesu anatenga Petulo, Yakobo ndi Yohane, n’kukwera nawo m’phiri lalitali, kwaokhaokha. Kumeneko iye anasandulika pamaso pawo,+
29 Pamene anali kupemphera, maonekedwe+ a nkhope yake anasintha ndipo chovala chake chinaoneka choyera kwambiri ndi chonyezimira.+