Yakobo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho gonjerani+ Mulungu, koma tsutsani Mdyerekezi+ ndipo adzakuthawani.+ 1 Yohane 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tikudziwa kuti tinachokera kwa Mulungu,+ koma dziko lonse lili m’manja mwa woipayo.+ Chivumbulutso 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo anamugonjetsa+ chifukwa cha magazi a Mwanawankhosa,+ ndiponso chifukwa cha mawu a umboni wawo.+ Ndipo iwo sanaone kuti miyoyo yawo ndi yofunika,+ ngakhale pamene anali pa ngozi yoti akhoza kufa.
11 Iwo anamugonjetsa+ chifukwa cha magazi a Mwanawankhosa,+ ndiponso chifukwa cha mawu a umboni wawo.+ Ndipo iwo sanaone kuti miyoyo yawo ndi yofunika,+ ngakhale pamene anali pa ngozi yoti akhoza kufa.