1 Timoteyo 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Usafulumire kuika munthu aliyense pa udindo,*+ kapena kugawana ndi anthu ena machimo awo.+ Pitiriza kukhala ndi khalidwe loyera.+ Chivumbulutso 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndipo ndinamva mawu ena kumwamba, akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake,+ ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.
22 Usafulumire kuika munthu aliyense pa udindo,*+ kapena kugawana ndi anthu ena machimo awo.+ Pitiriza kukhala ndi khalidwe loyera.+
4 Ndipo ndinamva mawu ena kumwamba, akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake,+ ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.