Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Akorinto 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Chifukwa panopa wina akabwera kwa inu n’kulalikira za Yesu wosiyana ndi amene tinamulalikira,+ kapena wina akakubweretserani mzimu wosiyana ndi umene munalandira kale,+ kapena uthenga wabwino+ wosiyana ndi umene munaulandira, inu mumangomulolera munthu woteroyo.+

  • Agalatiya 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndine wodabwa kuti mwapatutsidwa mwamsanga, kuchoka kwa Iye+ amene anakuitanani mwa kukoma mtima kwakukulu kwa Khristu,+ ndipo mwakopeka ndi uthenga wabwino wamtundu wina.+

  • Aefeso 6:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Valani zida zonse zankhondo+ zochokera kwa Mulungu kuti musasunthike polimbana ndi zochita zachinyengo+ za Mdyerekezi,

  • 1 Timoteyo 1:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mwana wanga Timoteyo, ndikukulamulira+ kuchita izi malinga ndi maulosi+ amene ananeneratu za iwe, kuti mogwirizana ndi maulosiwo upitirize kumenya nkhondo yabwino.+

  • 1 Timoteyo 6:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Menya nkhondo yabwino yosunga chikhulupiriro.+ Gwira mwamphamvu moyo wosatha. Anakuitanira moyo umenewu ndipo unalengeza momveka bwino+ zinthu zokhudzana ndi moyo umenewu pamaso pa mboni zambiri.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena