Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 6:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Chifuniro cha amene anandituma ine n’chakuti, ndisataye aliyense mwa onse amene iye wandipatsa, koma kuti ndidzawaukitse+ pa tsiku lomaliza.

  • Yohane 17:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Sindikupempha kuti muwachotse m’dziko, koma kuti muwayang’anire kuopera woipayo.+

  • 2 Timoteyo 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 N’chifukwa chake ndikuvutika chonchi,+ koma sindikuchita manyazi.+ Pakuti ndikudziwa amene ndikumukhulupirira, ndipo ndikukhulupirira kuti adzasunga+ chimene ndachiika m’manja mwake kufikira tsikulo.+

  • 2 Timoteyo 4:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ambuye adzandipulumutsa ku choipa chilichonse+ ndipo adzandisungira ufumu wake wakumwamba.+ Iye apatsidwe ulemerero mpaka muyaya. Ame.

  • 1 Petulo 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 inuyo amene Mulungu akukutetezani ndi mphamvu yake chifukwa muli ndi chikhulupiriro.+ Mulungu akukutetezani kuti mudzalandire chipulumutso,+ ndipo chipulumutso chimenechi chidzaonekera+ mu nthawi ya mapeto.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena