Mateyu 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Odala ndi anthu achifundo,+ chifukwa adzachitiridwa chifundo. Mateyu 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho pitani mukaphunzire tanthauzo la mawu akuti, ‘Ndikufuna chifundo, osati nsembe.’+ Chifukwa ine sindinabwere kudzaitana anthu olungama, koma ochimwa.” Yakobo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti wosachita chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo n’chopambana kwambiri kuposa chiweruzo.
13 Choncho pitani mukaphunzire tanthauzo la mawu akuti, ‘Ndikufuna chifundo, osati nsembe.’+ Chifukwa ine sindinabwere kudzaitana anthu olungama, koma ochimwa.”
13 Pakuti wosachita chifundo adzaweruzidwa mopanda chifundo.+ Chifundo n’chopambana kwambiri kuposa chiweruzo.