Yohane 6:69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 69 Ife takhulupirira ndipo tadziwa kuti inu ndinu Woyera wa Mulungu.”+ Machitidwe 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inde, inu munakana woyera ndi wolungamayo,+ ndipo munapempha kuti akumasulireni munthu wina, munthu wopha anthu.+ Aheberi 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti mkulu wa ansembe ngati ameneyu ndiyedi wotiyenerera.+ Iye ndi wokhulupirika,+ wosalakwa,+ wosaipitsidwa,+ wosiyana ndi anthu ochimwa,+ ndipo wakwera pamwamba kwambiri kuposa kumwamba.+
14 Inde, inu munakana woyera ndi wolungamayo,+ ndipo munapempha kuti akumasulireni munthu wina, munthu wopha anthu.+
26 Pakuti mkulu wa ansembe ngati ameneyu ndiyedi wotiyenerera.+ Iye ndi wokhulupirika,+ wosalakwa,+ wosaipitsidwa,+ wosiyana ndi anthu ochimwa,+ ndipo wakwera pamwamba kwambiri kuposa kumwamba.+