Yesaya 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzaika makiyi+ a nyumba ya Davide paphewa pake. Iye akatsegula palibe amene azidzatseka ndipo akatseka palibe amene azidzatsegula.+ Luka 1:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ameneyu adzakhala wamkulu+ ndipo adzatchedwa Mwana wa Wam’mwambamwamba.+ Yehova Mulungu adzam’patsa mpando wachifumu+ wa Davide atate wake.+
22 Ndidzaika makiyi+ a nyumba ya Davide paphewa pake. Iye akatsegula palibe amene azidzatseka ndipo akatseka palibe amene azidzatsegula.+
32 Ameneyu adzakhala wamkulu+ ndipo adzatchedwa Mwana wa Wam’mwambamwamba.+ Yehova Mulungu adzam’patsa mpando wachifumu+ wa Davide atate wake.+