1 Mbiri 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Usiku anali kukhala mozungulira nyumba yonse ya Mulungu woona chifukwa anali pa utumiki wawo waulonda.+ Iwo ndiwo anali kusunga kiyi kuti azitsegula zipata m’mawa uliwonse.+ Chivumbulutso 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Kwa mngelo+ wa mpingo wa ku Filadefiya, lemba kuti: Izi ndi zimene akunena woyerayo,+ amene ali woona,+ yemwe ali ndi kiyi wa Davide.+ Iye amene amati akatsegula palibe wina amene angatseke, ndipo akatseka palibe wina amene angatsegule.
27 Usiku anali kukhala mozungulira nyumba yonse ya Mulungu woona chifukwa anali pa utumiki wawo waulonda.+ Iwo ndiwo anali kusunga kiyi kuti azitsegula zipata m’mawa uliwonse.+
7 “Kwa mngelo+ wa mpingo wa ku Filadefiya, lemba kuti: Izi ndi zimene akunena woyerayo,+ amene ali woona,+ yemwe ali ndi kiyi wa Davide.+ Iye amene amati akatsegula palibe wina amene angatseke, ndipo akatseka palibe wina amene angatsegule.