Yesaya 26:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Inu Yehova, pa nthawi ya masautso iwo atembenukira kwa inu.+ Mutawalanga, akhuthulira mitima yawo kwa inu m’pemphero lonong’ona.+
16 Inu Yehova, pa nthawi ya masautso iwo atembenukira kwa inu.+ Mutawalanga, akhuthulira mitima yawo kwa inu m’pemphero lonong’ona.+