Genesis 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno ana a Mulungu+ woona anayamba kuona+ kuti ana aakazi a anthu anali okongola. Chotero, anayamba kudzitengera okha akazi alionse amene anawasankha. Yobu 38:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamene nyenyezi za m’mawa+ zinafuula pamodzi mokondwera,Ndiponso pamene ana onse a Mulungu+ anayamba kufuula ndi chisangalalo? 2 Akorinto 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho n’zosadabwitsa ngati atumiki ake+ nawonso amadzisandutsa atumiki a chilungamo. Koma mapeto awo adzakhala monga mwa ntchito zawo.+
2 Ndiyeno ana a Mulungu+ woona anayamba kuona+ kuti ana aakazi a anthu anali okongola. Chotero, anayamba kudzitengera okha akazi alionse amene anawasankha.
7 Pamene nyenyezi za m’mawa+ zinafuula pamodzi mokondwera,Ndiponso pamene ana onse a Mulungu+ anayamba kufuula ndi chisangalalo?
15 Choncho n’zosadabwitsa ngati atumiki ake+ nawonso amadzisandutsa atumiki a chilungamo. Koma mapeto awo adzakhala monga mwa ntchito zawo.+