Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 16:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pakuti Mwana wa munthu adzabwera ndithu mu ulemerero wa Atate wake limodzi ndi angelo ake. Pa nthawi imeneyo adzapatsa aliyense mphoto malinga ndi makhalidwe ake.+

  • Aroma 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Iye adzaweruza aliyense malinga ndi ntchito zake motere:+

  • Agalatiya 5:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndikukhulupirira+ kuti inu amene muli ogwirizana+ ndi Ambuye, simudzasintha maganizo, koma munthu amene amakuvutitsani,+ adzaweruzidwa+ kaya akhale ndani.

  • Afilipi 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Amenewo mapeto awo ndi chiwonongeko,+ ndipo mulungu wawo ndi mimba yawo.+ Ulemerero wawo uli m’zinthu zawo zochititsa manyazi,+ ndipo maganizo awo ali pa zinthu za dziko lapansi.+

  • 2 Timoteyo 4:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Alekizanda,+ wosula zinthu zamkuwa uja, anandichitira zoipa zambiri. Yehova adzamubwezera malinga ndi ntchito zake,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena