Chivumbulutso 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma bwalo lakunja+ kwa nyumba yopatulika ya pakachisi ulisiye, usaliyeze m’pang’ono pomwe chifukwa laperekedwa kwa anthu a mitundu ina.+ Ndipo iwo adzapondaponda mzinda woyera+ kwa miyezi 42.+ Chivumbulutso 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno ndidzachititsa mboni zanga ziwiri+ kunenera+ kwa masiku 1,260, zitavala ziguduli.”+
2 Koma bwalo lakunja+ kwa nyumba yopatulika ya pakachisi ulisiye, usaliyeze m’pang’ono pomwe chifukwa laperekedwa kwa anthu a mitundu ina.+ Ndipo iwo adzapondaponda mzinda woyera+ kwa miyezi 42.+