Machitidwe 20:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndipo pakati panu anthu ena adzayamba kulankhula zinthu zopotoka+ kuti apatutse ophunzira aziwatsatira.+ 2 Akorinto 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti amuna oterowo ndi atumwi onama, antchito achinyengo,+ odzisandutsa atumwi a Khristu.+
30 Ndipo pakati panu anthu ena adzayamba kulankhula zinthu zopotoka+ kuti apatutse ophunzira aziwatsatira.+