Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 8:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kenako anabweretsa nkhosa yamphongo yachiwiri, nkhosa yowaikira kuti akhale ansembe,+ ndipo Aroni ndi ana ake anaika manja awo pamutu pa nkhosayo.+

  • Levitiko 8:25-28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Atatero anatenga mafuta a nkhosayo, mchira wa mafuta, mafuta onse okuta matumbo, mafuta apachiwindi, impso ziwiri ndi mafuta ake ndi mwendo wakumbuyo wakumanja.+ 26 Mʼdengu la mikate yosafufumitsa limene linali pamaso pa Yehova, anatengamo mtanda umodzi wa mkate wozungulira woboola pakati,+ mtanda umodzi wa mkate wozungulira woboola pakati wothira mafuta+ ndi kamtanda kamodzi ka mkate kopyapyala. Anaziika pamwamba pa mafuta ndi mwendo wakumbuyo wakumanja. 27 Atatero anaika zonsezi mʼmanja mwa Aroni ndi mʼmanja mwa ana ake nʼkuyamba kuziyendetsa uku ndi uku monga nsembe yoyendetsa uku ndi uku yoperekedwa kwa Yehova. 28 Kenako Mose anazitenga mʼmanja mwawo nʼkuziwotcha paguwa lansembe pamwamba pa nsembe yopsereza. Zinthu zimenezi zinali nsembe yowaikira kuti akhale ansembe, yakafungo kosangalatsa.* Inali nsembe yowotcha pamoto yoperekedwa kwa Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena